Fighting Against Hiv/Aids and Sti

Fighting Against Hiv/Aids and Sti

Share

PHUNZILANI ZA HIV/AIDS NDIMATENDA OPATSILANA POGONANA MULI KUNYUMBA. UTHENGA WA CHIPATALA.PANGANI FOLLOW PAGE LATHU.
*ART AND STI CLINICAL MENTOR*

04/06/2026

Ati ndizoona zachitikadi ndipo ndayamba kumwa ma ARV. ine ndilibe problem.
Mzanga atuluka negative ngakhale akanisisa kuti banja lipitilile koma zimachitika. Ndilibe problem

04/06/2026

ife taona anthu oti ali ndi HIV kukhala mpaka kukalamba. nkhani ndi kumwa ma ARV mwandondomeko basi.

04/06/2026

post iyi yandikumbusa a dah ena ake amaopa kumwela kapu imene amamwela munthu wa HIV, worse enough mnthuyo anali owonda kwambiri nde ada awa amati apa straight utha kutenga HIV.
maonekedwe akhale apo. komasungatenge HIV kuzela ku kapu

04/06/2026

akasiiiii kumeneko bola mwamva

04/06/2026

Good morning.
Munthu atha kunena kuti ndimamwa ma ARV mwandondomeko,koma kuchipatala timadziwira ndi kuchepa kwa tizilombo ta HIV mthupi (Viral load). ndipo sitinamizidwa ngati pa chithunzipa m***a kudziwa mwini wake wa tayala

03/06/2026

Of course mzathuyu alakwisa kuthawa kuopa mantha.
koma pamenepo pamayenela kuoneka ma line awiri osati atatu.
nde wina ku comment section akuti ameneyo ndekuti *HIV yake ndiyamphamvu itha kumupha nthawi Ina iliyonse*
nkhani za HIV sizimayenda choncho.
komaso ngati sipakuonekaso line iliyonse dziwani kuti ndi invalid.

koma zothawa zosatila sizabwino tikumvana eti

03/06/2026

Dziwani kuti koyedzera kamkamwa kapena kakuchipatala kakamaonetsa mdzere pamene palembedwa T ngati pa C palibe kalikonse , imeneyo ndi invalid result kapena kuti si zotsatila zoona

03/06/2026

apa sizinayende .
Tikamayezetsa magazi pakuyenela pakhale line imodzi kapena awiri komaso ma line akhale pamalo ovomelezeka.
uyu amayenela abweredze koma akana ati akaganize Kaye. koma as it stand ndi invalid results.

03/06/2026

Big shout out to my newest top fans! Friday Knight, Beatrice Botha, Martha Martha, Bridget Happy, Ganizani Charles Mkakala, Emily Gwaza, Euriter Bello, Naomi Praise, Maunei Katseka, Loss Loss, Gift Victor Yambane, Madjozi Wisick, Regan Singini, Violet B Kanyada, Mary Wa Benard Favor, Elizabeth Wilson, A Nyachirwa Gome, Mtunduwatha Walas, Eliza Kamwendo, Emmore Alinafe Mawanga, Prai Se, Hlupe Mang'anda, Kingsley John Maloya, Edisher Sou Mah Ili, Charity Ntodwa, Chicco Chifundo, Naomi Nyirenda, Martha Lamya, Jose Abuba Kar Bandawe, Ell Nish, Mariam Mpondah, Mecy Maluba, Melody Mimo Sithembile Maphosa, Benson Kaunga, Daniel Nangwale, Sarai Chatha, Lostica Losbyb Nyadaufe Chirwa, Rhoda Wa Willard Ganeti, Ibraheem Nyebwazie Chimbayoh, Hp Sodzapanja, Akuchawo Major Kasupe

03/06/2026

Always make sure. Manyuchi Premium all the way. Order yours on WhatsApp at 0880 185 060

Want your business to be the top-listed Beauty Salon in Lilongwe?
Click here to claim your Sponsored Listing.

Telephone

Address

Lilongwe