Lilongwe UTM Vendors

Lilongwe UTM Vendors

Share

Contact information, map and directions, contact form, opening hours, services, ratings, photos, videos and announcements from Lilongwe UTM Vendors, Health/Beauty, Lilongwe.

20/07/2026

UTM ili ndi eni ake nde awawa omwe samatekeseka iwoo nganganga, wina akugona ife tikutenga boma 2030

Photos from Lilongwe UTM Vendors's post 14/07/2026

UTM ndi imodzi

13/07/2026

Mtchana alikomko

Photos from Lilongwe UTM Vendors's post 13/07/2026

UTM NEC MEETING

07/07/2026

zili ku office biggy sakugona tulo tiyeni timumve masanawa

07/07/2026

Behind central region Vendors kuli mkulu uyu yemwe ndi Chairman wathu Angunga (Raphael Tsabola) yemwe ndikatundu weniweni wa UTM zosakakamiza.

mkuluyu akati abangule pa msokhano aliyese amadziwa kuti machine atokota, uyu payekha ndi SKC kale.

mkuluyu anabadwa lero ndipo tikukondwerera birthday yake ndithu, ngati chipani tiyeni tikondwere naye limodzi.

01/07/2026

eeeeh

01/07/2026

kodaida izoooo

01/07/2026

eeeeh kwachematu

Want your business to be the top-listed Beauty Salon in Lilongwe?
Click here to claim your Sponsored Listing.

Category

Website

Address

Lilongwe