Frank POG Nsewa
Supporter Wazoona
17/07/2026
Osewela mpila wa miyendo khuda Muyaba tsopano ndi osewela amene akulandila ndalama zambili pa osewela onse mu league yaikulu ya kuno ku Malawi .
Khuda amene pano ndi osewela wa timu ya Masters FC ali pa nambala 1 ndipo wachiwiri ndi osewela wa timu ya Ekhaya fc Alick Lungu amene amalandila ndalama zosachepela K1.5 million pa mwezi.
Mukuona kuti Muyaba amene ali pa nambala 1 akutapila zingati pa mwezi ku Masters FC?
16/07/2026
Waleroπ²π¦ vs π²πΌ
16/07/2026
SULOM has announced the names of players and officials who are suspended and will miss the upcoming weekend matches.
15/07/2026
π¨ ππππππππ: FIFA will break football laws at the World Cup final on Sunday, according to The Times. π
The half-time break will last up to 30 minutes to accommodate the half-time show. β³
15/07/2026
Nduna ya zamasewelo Alfred Gangata ali pambuyo pa England usiku uno.
'' My people football England England'' said Gangata via His FB account.
15/07/2026
Malingana ndi nyumba yolemba nkhani zamasewelo ya The Daily Mail Oimbila amene ayimbile masewelo apakati pa timu ya England komaso Argentina IsmaΓ―la Elfath amakonda Lionel Messi ndipo GOAT sagonja masewelo amene iyeyu wayimbila.
Elfath anali othandizila ma final amasewelo apakati pa timu Argentina ndi France mu 2022 ampikisano wa FIFA World Cup komanso anaimbila final ya league Cup ku America ndipo inapambana ndi timu ya Lionel Messi ya inter Miami.
Elfath waimbila masewelo 4 a timu ya Lionel Messi chipitileni ku America osewelayi ndipo Messi wapambana masewelo onsewa.
Ziliko tu π
13/07/2026
Karonga United π²πΌ
TODAY'S FIXTURES
WORLD: World Championship - Quarter Finals
22:00 France - Morocco
EUROPE: Europa League - Qualification
18:00 Qarabag - Vestri
19:00 Dyn. Kyiv - U. Cluj
19:00 Sheriff Tiraspol - Aluminij
20:00 CSKA Sofia - Derry City
20:00 Hajduk Split - Zilina
20:00 Vojvodina - Ferencvaros
EUROPE: Conference League - Qualification
16:00 Atletic Escaldes - Mornar Bar
18:00 Alashkert - Yelimay Semey
18:00 Dila Gori - Virtus
18:00 FK Liepaja - Decic
18:00 Hegelmann - Paide
18:00 Kalju - Linfield
19:00 Bohemians - St Josephs
19:00 Din. Minsk - Sileks
19:00 Marsaxlokk - Pyunik Yerevan
19:00 Velez Mostar - Milsami
19:15 Mondorf - Dinamo Tbilisi
19:30 Caernarfon - Levadia
19:30 Europa FC - Shkendija
20:00 Vllaznia - Malisheva
20:30 Glentoran - RFS
20:45 NSI Runavik - Hamrun
20:45 Penybont - FC Santa Coloma
20:45 Petrovac - Zalgiris
21:00 Dinamo Tirana - FC Astana
21:00 FK Sarajevo - Inter Turku
21:00 Stjarnan - Vikingur Gota
Frank POG Nsewa
07/07/2026
weekend uyaka Airtel top 8
Full Time
United States 1-4 Belgium
USA have been knocked out of the tournament ndipo Balogun anasewela koma Belgium yachita nkhaza.
Tidikile kuche tione kuti atate awo Trump anena kuti chani koma paja anakamba kale kuti ngati agonje ndi Belgium kukhala kuti awabela.
Click here to claim your Sponsored Listing.
Website
Address
Lumbadzi
