Ungwazi

Ungwazi

Share

Nasanganya wazinthu
kuchimpwilikiti
kumpanipani kwenikweni

Photos from Ungwazi's post 17/07/2026

Kho ndi Chloe anthu awawa anali paubwezi wamseli ndithu coz no momwe amakonderana kupangira limodzi ma video aja sangangofikira ponyambana choncho chifukwa chamaliro abolo ndikutha kuwona kuti mwina pamayenda chiperekanyu chidyerano mwina nthawi iyiyi amayenera kuti azilimbitsana mtima not kupanga zimenezi munthu kuyikidwa Manga week siyinathe ndikomwe🙌🏽


Ndikuzeniko inu muwonapo bwanji?

Follow Ungwazi timve nawo

17/07/2026

Koma anaba chani kuti mpka afike powalanga chonchi abale🙄


Follow Ungwazi

16/07/2026

Komatu pena anthu obwerafe tikati tipangitse manyazi🙌🏽
Ati kupanga comment pa video yawapolice ati ndilibe ma documents momwe amutukwanira anthu akuno🙌🏽




Follow Ungwazi for more🤗

15/07/2026

I just like this movie🤗💕
EMEKA IKE is back again 💞





Follow Ungwazi for more

15/07/2026

Kuvuka nachilungamo😝😝




Follow Ungwazi

14/07/2026

Anthu aku Congo apha truck driver waku South Africa koma chipongwe tikubwezera kwaanthu osalakwa osamayiwala kuti anthu aku themba sionse oyipa mitima makamaka omwe amayenda yendawa ndiabwino chifukwa amaziwa kuti nafeso tinapita mayiko aeni koma osayendawa ndevuto💔





Follow Ungwazi for more

14/07/2026

Video iyi ndiyaanthu omwe alikutheba ndiomwe ali kumalawi akufuna kubwera kuno tiyeni tisamale tisangopeleka ndalama kwanthu mudzina loti akutipangira ma paper please 🙏🏾


Follow Ungwazi

13/07/2026

Chonde mundimvetsese ndanena kuti amene akufuna chifukwa palibe chomwe ineyo mutandipase so please osabwera direct ku inbox kutha mawu chonde🙏🏾ndikufuna kupanga share maganizo chifukwa Malawi wina wadyeredwa ndalama yomwe anatsala nayo kuti azipitira kumalawi ndewina ananena kuti amupangire chi pepala nkumupangira cha fake munthu wagwidwa apapa akumutumiza ku lindera ndezangondimvetsa chisoni mpake ndikufuna kungopanga share zomwe mungatsatire zitengera kwaomwe akufuna chifukwa🤗

13/07/2026

Kwaamene mukufuna kukhala mu South Africa mwaufulu you can follow zomwe ndinganene simundipasa ndalama koma i can help you zomwe ndinapanga ineyo kwaomwe amatha kupanga follow bwino munthu akawauza zochita panopa anthu akubera anthu kuti akupanga ma paper anthu asakunamizeni pliz panopa anayima kaye kupanga ma paper ineyo ndinapitako ndekha kukafunsa ndipo I will share zomwe tingapange mwina zingathandize panopa amalawi akubera amalawi anzawo posamverana chisoni kuti nyengo sizili bwino osapeleka ndalama kwamunthu kuti akupangire work permit please 🤗 wishing you all the best💞

Follow Ungwazi for more

13/07/2026

Good morning



Follow Ungwazi

Want your business to be the top-listed Beauty Salon in Mzimba?
Click here to claim your Sponsored Listing.

Category

Website

Address

.. .
Mzimba
......