ibn ja'far
to grow up our communication with Allah
12/08/2026
Amene munatsilikapo munda, nyumba, shop, ndalama, kapena chilichonsecho jannah simukainvera ngakhale fungo
paja kutsilika ndi shirk yaikulu
ndipo tchimo lomwe Allah samakhululuka ndilo la shirk
munatsilika kalekale kwambiri ndipo simukupempha chitetezo kwa Allah chifukwa mukudalira zithumwazo
pogona simupanga ma Dua mukudziwa kuti munakonza kale
zonvetsa chisoni kuti munayika zimenezo zikukutetezani ndithu koma mukadzuka mmamawa mukumapita ku swalaat ya Fajr
mumamukonda Allah koma simumamukhulupirira kuti akhoza kuteteza zanu zonse
masamu mukupangao mngachabe
Ndipo mpaka sheikh akuyenda ndi zithumwa waku bizinezi akuopa wachitaka ngakhale wavala mkanjo akuchokera ku mzikiti.
sindikuti ntchito zabwinozo musiye ayi. koma ndikukumbutsani kuti choyamba chotsani nyasinzo kenako mulape kwa Allah kuti ntchito zanuzo zikhale zonunkhira
muzitolere!!
09/08/2026
funso
Eti zafika pomafusa kuti nkhondoyi wawina ndi ndani kkkkk
koma ma super power enawa
Koma kwabuka ti ma sheikh pa social media mmmmm
05/08/2025
ad-dajjal uja aku trenda uku takaoneni
TikTok · ibn ja'far 6279 likes, 442 comments. “dajjal part 1”
Dajjal part 1
I'm ready
Are you ready for ?
Click here to claim your Sponsored Listing.
Category
Website
Address
Salima
Alerts
Be the first to know and let us send you an email when ibn ja'far posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.
