The Lokas Delivering Smiles
The Lokas is a trusted couple dedicated to delivering thoughtful and personalized gifts to friends
29/07/2026
๐ฅ| Mwana wa Chemwali anga Ellena deserves fresh flowers and some cash. Mupite ku Area 25 mukandithokozere, ndi mwana otumika komanso omvera, samanyinyilika komanso amayangโanira bwino azibale ake. Tapanga zomwe anatituma๐บ๐บ
Congrats Ellena and enjoy the day ๐๐๐
Thanks DRdee NyaChirwa for trusting The Lokas Delivering Smiles ๐๐๐
Mlamu olandira bwino alendo dzulo wadalitsika ndi DRdee NyaChirwa ๐๐๐
Thanks for trusting us๐๐ป๐๐ป
27/07/2026
Mlamu odziwa kulandira bwino alendo๐๐๐ receive your flowers Aunt Charlene Chisema. Akuchimuna amakumyadirani ati chifukwa ndinu munthu osazikonda๐๐๐๐๐
Thanks DRdee NyaChirwa for trusting us to deliver an appreciation gift to your brothers wife๐๐ป๐ผ๐ผ
We delivered Fresh Flowers and Cash๐ธ
The Lokas Delivering Smiles ๐๐ฅ๐ฅ๐ฅ
27/07/2026
Sunday duties ๐๐ | Odi odi kuno๐ผ๐ถ๐ถ takamupeza ku Bridal Shower๐คฃ๐โโ๏ธ
Yesterday, we had the privilege of surprising Sharom with an appreciation gift from DRdee NyaChirwa in recognition of her selflessness, kindness, and loving heart.
We presented her with a beautiful bouquet of fresh flowers and a cash gift. This gesture was a small way of acknowledging the positive impact she continues to make through her compassion and generosity.
Thank you, Sharom, for being an inspiration. Your kindness does not go unnoticed, and we celebrate the remarkable person you are.
Aunt Dannas is back and this is her birthday week๐๐๐๐๐๐๐
Thank u for 10K followers๐๐ป๐๐ป
Alendo ndi ati ? Tikulandireni๐บ๐บ๐คฃ
23/07/2026
โNdikamawaona akazaka ndimayamika kumwamba chifukwa choti ndinatola Joker, mkazi oti zikandivuta amamvesetsa, mkazi oti olo abale anga amawathandiza even ineyo ndisakudziwa.
โLero ndi tsiku lomwe anabadwa ,mupite mukandithokozere, mukamuuze kuti kupezeka kwake mโmoyo mwanga ndimathokoza Chauta๐๐ป๐๐ป.โ
Thanks Dr. Thoko Kapalamula for trusting The Lokas Delivering Smiles๐๐ฅ๐ฅ๐ฅ
Happy Birthday Aunt Natasha, amunanu amakonyadirani koopsaโค๏ธโค๏ธ๐๐
Inu mutituma liti? 0995108693โ๏ธ
21/07/2026
Lero nyimbo ikhale โiye anabala mwana ali ndi nzeru๐ถ๐ผโ Odii odii kuno ibwere pambuyo๐๐๐๐ฅ๐ฅ๐ฅ๐ฅ.
Tiwonge Mkazimzungu DeMond yemwe ali ku America wagulira makolo ake Galimoto ngati njira imodzi yowathokoza pomulera bwino komanso kusamala bwino ana ake pamene iye ali ku Magobo๐น๐น.
We also delivered fresh flowers as a symbol of Love from the Daughter๐๐๐๐๐ป
Mr. and Mrs Mgomezulu landirani Maluwa anu๐น๐น๐๐
21/07/2026
โNgakhale ndi achimwene awo zinthu sizinayende koma tinapanga ubale, she is now like a sister, amandilimbikitsa munjira zambiri, mupite mukandithokozere adziwe kuti ndimamunyadira,โ
chilamu sichitha, Priscah trusted us to deliver a surprise birthday gift to her Ex Mlamu
Delivery made simple, love made visible๐๐๐
The Lokas Delivering Smiles ๐ฅ๐ฅ๐ฅ๐ฅ 0995108693
Yesterday The Lokas Delivering Smiles inayendera mnyamata ochokera mโmudzi mwa Kachipeya,mfumu yaikulu Kachere mโboma la Dedza.
Angakhale kuti sanafike zaka 40 , mnyamatayu ndi mwini wake wa Masters Group of Companies yomwe mkati mwakemo muli ma kampani osiyanasiyana kuphatikiza yachitetezo komanso team yampira wa miyendo yotchedwa Masters Football club.
Kudzera mu ma kampani amenewa mnyamatayu wapereka mwai watchito kwa a Malawi ochuluka.Iyeyu amachitanso ntchito zachifundo monga kuthandiza amasiye komanso okalamba.
Chifukwa cha masomphenya komanso kulimba mtima kwake, mnyamatayu anapatsidwa udindo okhala Vice president wa Chipani Cholamula cha DPP mu chigawo cha pakati.
Iyeyu anakhalaponso Minister of State, kenako anazasankhidwa kukhala Minister of Natural resources ndipo pano ndi Minister of Sports and Culture.
Ifeyo zoti life begins at 40 tatsutsa ndipo moyo umayamba ukalemba masomphenya ako ndikuyamba kuwatsatira๐๐ป๐๐ป๐โโ๏ธ๐โโ๏ธ
Pitilizani kulimbitsa mtima achinyamata kuti ndi zotheka๐ฅ๐ฅ
Receive your Flowers with Power Hon.Alfred Gangata๐๐ป๐๐ป๐๐ป๐๐ป๐๐น๐
Click here to claim your Sponsored Listing.
Category
Website
Address
Cape Town
7560
