Ungwazi

Ungwazi

Share

Nasanganya wazinthu
kuchimpwilikiti
kumpanipani kwenikweni

11/07/2026

Akuti uyu ndi Adam waku Tanzania anachita ngozi ndipo anadulidwa miyendo yonse tiyamike Mulungu alimoyo chofunikira kwambiri ndimoyo🤗magaye ukakhala paulendo nakafika bwino chonde osamayiwala kuyamika sikuchenjera koma ndichisomo Mulungu amakonda aliyese tiyeni tizipemphelerana🙏🏾





Follow Ungwazi with your love💞

11/07/2026

Post ma meme tiyike nawo ku status kuli empute

10/07/2026

Kodi awawa pa social media amangokhalira kuukira kenako kungosokoneza anthu basi? Ineyo kuchokera momwe ndinayambira kuwona ma post a Asher amangokhalira kunyoza anthu basi apapa akusonkhozera moto wa Max & Sherry Dine and Lounge ndi Chris Loka anthu ena amabisalira kupanga zoyipa mzina loti ndipa social media mumayiwala kuti anthu udani omwe mumawapasira umakhala weniweni mwina vuto ndineyo sizakundikomerane?

Ungwazi

10/07/2026

Achizimayi okhaokha yisakhaletu yilisanje Doctor Favour kungogwira ntchito 5 months zowona abale kulimbikira sukulu pachabe munthu kulakwatu uku😭




FOLLOW Ungwazi FOR MORE

09/07/2026

Koma anthu mukuyankhura bwanji?
Akuti anthu mukungolira koma nkazi wake weniweni sitikuziwa kuti ndiuti show yeni yeni 🙌🏽kokawona nkhope maliro a

09/07/2026

Eti ndizowona izii? Kwaomwe mumakwera nawo ma bus a ulele tiuzeniko🤗





FOLLOW Ungwazi

08/07/2026

Ndiuzeniko iyiyi yinandiponya zikuti bwanji kodi zama surprise?

08/07/2026

Nanga amalawi angapange zimenezi koma tiwona zinthu😝😝ndasiyira p***a kupanga order zakudya kwama delivery boy😝😝



Follow Ungwazi for more

08/07/2026

Kusiya ma secretly widow sate🙌🏽Boys muli very dangerous 🙌🏽😝😝uyuu chikumudza kuti you're my only one wina chikuti unandidyetsa kondaine wina I will die for you 😝😝 akulowa live azimayi ma content nkati 😝
Koma moyo winawo osazapangaso zimezo🙌🏽




Ungwazi

08/07/2026

Amene tilindikangachepe tiyeni tizikakwera kaya ndalama yikathera pa dedza bola tasuntha malo ngati awa ndi weather yake yimeneyi kumangodikira titha kupezeka kuti tadwala nazo🙌🏽
Ena akumachita kunena kuti ine sindingalipire bus ndikwera zaulele koma ndalama alinayo🙌🏽





FOLLOW Ungwazi

Want your business to be the top-listed Beauty Salon in Mzimba?
Click here to claim your Sponsored Listing.

Category

Website

Address

.. .
Mzimba
......