MR 3 B

MR 3 B

Share

LOVE CONNECTOR AND OTHER GOOD STORIES wapp me on +265888545597

29/05/2026

Mkazi oyika ndolo pamphuno sandisangalasa

Good night all

29/05/2026

Hello Mr 3b mwaswera bwanji chonde muwauzeko anyamata Anu k*ti sitonse amene timabwelera hit And run zandikwana zomalowa ku inbox kumandiuza za hit and run pomwe anthu ofuna hit and run amawaona mukupanga post chonde chonde pa social media sitinabwele kuzapanga uhule enafe

Vitu Wa Phiri

29/05/2026

NtsIkana wazaka 27 alibe mwana amakhala kwa Chinsapo 1 ku Longwe amapanga business yokhazikika

Àkufuna mwamuna amene alibe mkazi ndipo àkufuna mkazi wa serious k*ti akhazikike naye apange zabanja

Mayi wabwino safuna zongovula ai Koma kukhazikika ndimunthu mmodzi

Ndipezeni pa 0888545597

29/05/2026

Mr 3b, ine ndikufuna ndithokozeko Mrs eliza daud pondithandiza ndindalama yokwana k3000 . mulungu azipitiliza kuwadalitsa ndikukwanilisa zosowa ndi zokhumba pa moyo wawo.

29/05/2026

Pa post ya rent ija ndik*thokozaa a grey chilombo andithandiza ndi 10,000

lne Pretty

29/05/2026

*If you are chasing malawians also me am going with them to malawi because i love them*

*Muzulu ak*tero uku*

*Ngati muk*thamangisa amalawi ineso ndikupita nawo ku Malawi chifukwa ndi anthu abwino kwambiri ndipo ndimawakonda* 🤓

Amalawi savuta pa ndalama🤣

29/05/2026

Ak*ti nawo sizikuyenda koma amangoipasa moto page yi

Photos from MR 3 B's post 29/05/2026

Pepani kwambiri nakulemberani usiku message, munthune nathedwa nzeru and chonena chikunisowa k*ti nitani munthune,dzanalo ninabwera kuzapempha thandizo lamwana k*t wabinya mkono ninapita naye kuchipatara zinatheka ndalama ninabwereka,koma zachisoni leroli mwana yemwe uja mwendo anatelera nikugwa ndikunena pano wayamba k*tupa ine pogwira paliponse nilibiretu pano, nikupempha ma brothers, sisters chonde anithandizeko kumbali ya transport mawa nipite naye Ku mzuzu central, ndikupenpha K10,000
Zikatheka akupasani inuyo uncle

Ndiaja ankati # yawo yabloka pin

ngsti mukufuna kuwathandiza ndipezeni pa 0888545597

29/05/2026

Tatchulani komwe mumakhala mwina mukhonza kupeza wakufupi ndikwanuko mkupeza okuyenderani week end Yi

Mutchule boma ndi town yomwe muli

29/05/2026

MR 3 B

Kodi muthu akabeledwa fon zimatheka k*t ipedzekeso

Muthandizeni sister wathu uyu amakhala BT Machinjiri

29/05/2026

Ok ok thank you for giving me chance to speak, I don't know if it's write to ask you about this , but I need certain h**p ,first of all,IAM students at unima , we almost closed today semister 2, but I waiting month for transport, which possible I will go Monday but to be honest right now , I don't have relish ,I did try to borrow so that I can return once akanditumizira koma it didn't work in my favour, I don't know what to do any more,and more over people are leaving for holiday .to be honest things has been hard at latery at end of this semester, if you have any h**p I could reary appreciate ,or I can do any work like invite people to your page or anything. But if you don't have ,that's okay no worry, I will see way forward,if you need proof ,I can give. And lastly IAM very sorry, for asking you, IAM just disturbed not knowing way forward ,and IAM first year.thank for your time

Want your business to be the top-listed Beauty Salon in Blantyre?
Click here to claim your Sponsored Listing.

Category

Website

Address


BLANTYRE
Blantyre