GRAND VOICE YM2

GRAND VOICE YM2

Share

Grand voice sound

11/10/2022

Nthawi zina ndibwino kumayamikira zinthu zikakhala bwino
Ndiye ine ndimati nditele kuti

Iyiyi ndi couple mbambande ,

Prophet Shepherd Bushiri ndi Bushiri amakhala mmoyo osangalala mu nchikondi Chao, malingana ndi momwe ndimaonera tiyeni ku comment section tipange post tili ndi achikondi athu 😊

03/07/2022

πŸ‡²πŸ‡Ό
Pomafika chaka chΓ‘ mawa
Nafe tifika apaπŸ’΅pa matrllion pepala limozi
Ndiye kuti tikhala olemela thonseπŸ˜‚πŸ˜‚πŸ˜‚πŸ˜‚πŸ˜‚

Osaiwala kupanga LIKE Page πŸ‘

01/07/2022

Theba yafikano
Poyaluka Nanga izi ndi zichani
πŸ˜‚

Osaiwala kupanga LIKE Page

23/06/2022

SOUTH AFRICA πŸ‡ΏπŸ‡¦
President ramaposa Walesa kuvala
Mask 🎭 akuti Corona watha
Ndiye wina and palamule dΓ‘la siulowa muno opanda mask
Undinva cha munsa mtalowa kale

Osayiwala kupanga LIKE Page πŸ‘

18/06/2022

MUTIUZA BWINO
ZITHEKA BWANJI BLACK OUT THE WHOLE MALAWI πŸ‡²πŸ‡Ό????????

15/06/2022

Ntchito ndi zambiri
Nanga uncle wa amagwira ntchito yanji?????🀣🀣🀣🀣🀣🀣🀣🀣🀣

Osayiwala kupanga LIKE Page πŸ‘

14/06/2022

OZIWA MWAZIWA TIUZENI MUTI CHANI??? πŸ˜‚πŸ˜‚πŸ˜‚πŸ˜‚

09/06/2022

CHENJEZO β›” β›” β›” β›” ⚠️⚠️⚠️⚠️

ENA MUKUTSUTSA. NANGA IZI
NDALEMBA NDINE

NOTED
OSAYIWALA KUPANGA LIKE PAGE πŸ‘

Want your business to be the top-listed Beauty Salon in Lilongwe?
Click here to claim your Sponsored Listing.

Telephone

Address


Lilongwe