Kuwala Optics
Optical and eye care services. High quality at low cost.
MOTHER'S DAY
π
Open 08:00 am
Close 02:30 pm
12/10/2026
π MOTHER'S DAY PROMOTION π
(13 to 19 October)
Pokondwelera anakubala athu, tabweleretsanso ma discounts aja. K10,000 yochotsera pama glasses ena aliwonse π₯³
Mukagula ma glasses pompo mumalandiranso zinthu izi;
1. Spectacle case
2. Lens cleaner
3. Lens wiper
Prices: K55,000 to K89,000 π
Kuyeza maso ndi ulere. Ma glasses amakonzedwa pompopompo.
[Premium and Executive frames available]
LILONGWE: KIMS Building, Bwaila Hospital Road.
BLANTYRE: Al-amin Arcade, opposite AXA.
AREA 25: Nsungwi, after Matabwa market.
Call/Whatsapp: 0990511960
01/10/2026
NEW LOCATION
Lilongwe (Area 2) Shop panopa yasuntha ikupezekera malo ena π
Malo akale: Area 2, Opposite National Bank.
Malo atsopano: Area 2 yomweyo, mu KIMS Building, along nseu opita ku Bwaila Hospital.
Tikangokhota nseu opita ku chipatala cha Bwaila, tili mu Building yoyambilira, ndipo mukaonapo banner yathu yolemba KUWALA OPTICS.
Building imeneyi (KIMS) ndi momwenso muli a VICTORY Shopping Center komanso FRONT VIEW Cake Shop π
Call/Whatsapp: 0990511960
20/09/2026
AD-HOC DISCOUNTS
(Up to 03 October)
Mu nyengo ino yama Ad-hoc Committees, ife tabweretsa ma Ad-hoc Discounts pama glasses athu onse motere;
(A). Ma glasses ena alionse tachotsera K10,000 π₯³
(B). Ma glasses alionse a transparent frame tachotsera K15,000 π₯³
Mukagula ma glasses, timaperekanso zinthu izi mwaulere kuti mukasamalire ma glasses anu;
1. Spectacle case
2. Lens cleaner
3. Lens wiper
Prices: K55,000 to K85,000 π
LILONGWE: Opposite National Bank, Area 2.
BLANTYRE: inside Al-amin Arcade, opposite AXA.
AREA 25: Nsungwi, after Matabwa market.
Call/Whatsapp: 0990511960
24/08/2026
YABWERANSO PROMOTION
(Up to 05 September)
Eya, ma discounts ama K10,000 aja afikanso on all glasses. Mukagula ma glasses, pompo mumalandiranso zinthu izi;
1. Spectacle case
2. Lens cleaner
3. Lens wiper
Kuyeza maso ndi ulere. Ma glasses amakonzedwa pompopompo.
Mitengo: K49,000 to K85,000 π
[Premium and Executive frames available]
LILONGWE: Opposite National Bank, Area 2.
BLANTYRE: inside Al-amin Arcade, Opposite AXA.
AREA 25: Nsungwi, after Matabwa market.
Call/Whatsapp: 0990511970
19/08/2026
CONGRATS π
Biggy Ibrahim Stonard , inu mwapeza 29 likes pa comment yanu. Bwerani muzazipatse nokha discount, mene inu muzafunire popanda choletsa π
Suit mwavalayo, nde muikepo ma glasses pompo π Kuwala kokhakokha.
17/08/2026
MY PEOPLE GLASSES
Ma set awa ali pa K95,000 yokha. Clean sets π
Discount pang'ono, zikumatheka kugula at K89,000 π
Komano apa we need mmodzi abwere azagule pa discount yodzipatsa yekha. Kuzichotsera yekha mene wafunira, popanda choletsa π€£
Akhale ndani? Comment with more LIKES wins the chance π
[You can tag friends as many as you want. No zigoba accounts]
06/08/2026
NEW & RESTOCKED
Munawakonda, nde apa tawabweretsanso, ndamenewa. Available in all our shops. Only at K55,000 to K95,000 for full set π
Mukagula ma glasses, mumalandiranso zinthu izi;
1. Spectacle case
2. Lens cleaner
3. Lens wiper
Ma glasses amakonzedwa pompopompo. Kuyeza maso ndi ulere π
[Premium and Executive frames available]
LILONGWE: Opposite National Bank, Area 2.
BLANTYRE: inside Al-amin Arcade, opposite AXA.
AREA 25: Nsungwi, after Matabwa market.
Call/Whatsapp: 0990511960
23/07/2026
GULURA MONTH-END PROMOTION
(Up to 08 August)
Timalize stock imeneyi, tibweretsemo ena. Discount phwamwamwa π₯³
Lipirani K49,000 yokha pama glasses ena aliwonse omwe mtengo wake weniweni sukudutsa K69,000 π₯³
[All glasses at/below K69,000 are now selling at K49,000 only]
As usual, timaperekanso zinthu izi kwa onse omwe agula ma glasses;
1. Spectacle case
2. Lens cleaner
3. Lens wiper
Ma glasses amakonzedwa pompopompo. Kuyeza maso ndi ulere π
[Premium and Executive frames available]
LILONGWE: Opposite National Bank, Area 2.
BLANTYRE: inside Al-amin Arcade, opposite AXA.
AREA 25: Nsungwi, after Matabwa market.
Call/Whatsapp: 0990511960
16/07/2026
CONGRATULATIONS π
Ms MΓrrΓΓ© Γm Magombo and Mr. Jack Tombolombo zatengeni your Kuwala Packages, mwaiphula π₯³
NOTE: The instruction was kuti tinene zimene mnzathu wapakamwa uja anganene atakuonani kuti mwavala Kuwala Package for the first time π Nde some people had more Likes, koma they had not responded to the instruction.
Congrats Mirrie and Jack! π₯³
Click here to claim your Sponsored Listing.
Category
Telephone
Website
Address
Area 2
Lilongwe
Opening Hours
| Monday | 08:00 - 16:30 |
| Tuesday | 08:00 - 16:30 |
| Wednesday | 08:00 - 16:30 |
| Thursday | 08:00 - 16:30 |
| Friday | 08:00 - 16:30 |
| Saturday | 08:00 - 14:00 |
Alerts
Be the first to know and let us send you an email when Kuwala Optics posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.
