Healthy Herbs Clinic

Healthy Herbs Clinic

Share

Contact information, map and directions, contact form, opening hours, services, ratings, photos, videos and announcements from Healthy Herbs Clinic, Health/Beauty, T/A Njolomole, Ntcheu, Lilongwe.

31/05/2026

Amathana ndimavuto awa

1. Kuyiwala pafupipafupi
2. kusowa tulo
3. mutu waching'alang'ala
4. khunyu
5. kukhumudwa, and all brain related disorders

120 tablets at k45,000 only

*Healthy Herbal Care 🍀*

31/05/2026

*SHIGRU HIMALAYA TABLETS*

*Ma tablets omwe amachiza matenda osiyana siyana pa thupi.*

1. kupweteka kwa miyendo
2. Kuchiza Gout
3. Kuthandiza stroke
4. Kuchiza nyamakazi
5. Kuthana ndi ululu komanso kulimbitsa mafupa
6. Kuchiza kufufuma/kutupa kwa phanzi komanso manja
7. Kuchiza kufufuma kwa miyendo
8. Kuchiza mabondo ndi malo onse olumikizirana mafupa
9. Kuchiza kuotcha Kwa mapazi/manja/miyendo
10. Kuchiza matenda kutha Kwa ma Disc komanso ma cartridge
11. Kuchiza matenda amu spinal cord

Mtengo wake ndiK40,000

*Mukhoza kupeza ma product(mankhwala/ ma herbal) anthu onse kuno ku Lilongwe, ku Mzuzu, Jouburg, ndi ku Capetown(George) South Africa*

Mzuzu +265 991 22 35 78 (Miss T Muvalo)

Juburg Jewel City pafupi ndi Jeppe Train Station +27 63 303 8012 (Brighton)

Capetown (George)
Mrs Allan +27 81 233 7686

*Healthy Herbal Care ☘️*

31/05/2026

*MENOSAN TABLETS*

Azimayi aja simupanga period aja, herbal yanu ndi iyi:

Menosan is an exclusive herbal formula that helps women combat the occasional challenges associated with menopause. It promotes physical and emotional well-being in menopausal and post-menopausal states, as well as helping with occasional mood swings, insomnia, irritability and fatigue often reported by women.
---------------------
---------------------
Menosan ndi mankhwala azitsamba okhawo omwe amathandiza amayi kuthana ndi zovuta zanthawi zina zomwe zimadza chifukwa cha kusintha kwa thupi(kusapanga period) . Zimalimbikitsa kukhala bwino kwa thupi ndi maganizo m'madera otha msinkhu komanso pambuyo posiya kusamba, komanso kuthandizira kusinthasintha kwa nthawi zina, kusowa tulo, kukwiya komanso kutopa zomwe nthawi zambiri zimanenedwa ndi amayi.

Mankhalawa kwambiri anathandiza monga.
* Kusapanga msambo (period)
* Period yowawa
* Kubwezeretsa michere ya mthupi (hormones)

*Mukhoza kupeza ma product(mankhwala/ ma herbal) anthu onse kuno ku Lilongwe, ku Mzuzu, Jouburg, ndi ku Capetown(George) South Africa*

Mzuzu +265 991 22 35 78 (Miss T Muvalo)

Juburg Jewel City pafupi ndi Jeppe Train Station +27 63 303 8012 (Brighton)

Capetown (George)
Mrs Allan +27 81 233 7686

*Healthy Herbal Care ☘️*

31/05/2026

*V-Gel HIMALAYA CREAM*

K35,000 only

Mafuta ozoletsa ku ndata kuchotsa ma bacteria.

1. Amachotsa ma bacteria
2. Amachotsa yeast infections
3. Kuchotsa white discharge
4. Kuchotsa ma STIs
5. Kuchotsa zonyukha Ku ndata
6. Kuchotsa sungu ku malo obisika
7. Kuchiza kupweteka pa nthawi yogonana .
8. Kuchotsa mawuka
9. Kuchiza mabomu,chindoko
10. Kutsegula ma fallopian tube
11. Kuthana ndi zizindikilo za cancer ya mchiberekero.

K35,000

*Dzolani morning and evening*

*Mukhoza kupeza ma product(mankhwala/ ma herbal) anthu onse kuno ku Lilongwe, ku Mzuzu, Jouburg, ndi ku Capetown(George) South Africa*

Mzuzu +265 991 22 35 78 (Miss T Muvalo)

Juburg Jewel City pafupi ndi Jeppe Train Station +27 63 303 8012 (Brighton)

Capetown (George)
Mrs Allan +27 81 233 7686

Healthy Herbal Care ☘️

31/05/2026

*KUPEMPHERA*

*POSITION WHEN PRAYING(Mitundu yakakhalidwe popemphera)*

CHOKWEZA MANJA (1 Timothy 2 v 8).
>Uku ndikusonyeza kugonja pamaso pa Mulungu surrendering everything to him inu mukule ambuye ine ndichepe baba.

CHOIMILIRA ( Marko 11 vs 25)
>Kusonyeza kuti; wakonzeka kumenya nkhondo through prayer, fighting the devil and it also shows ndilipano ambuye ndakonzeka nditumeni( Daniel 1 vs 5).

CHOYANG'ANA KUMWAMBA ( Psalms 121 vs 1-2).

>Kusonyeza kuti; wakhulupilira Mulungu kuti mayankho achokera kumwamba kwa iye osati kwina kulikonse (Yohane 11 vs 41 - 42).

CHOWELAMA ( Exodus 34 vs 8).
>Uku ndikusonyeza ulemu kwa Mulungu ndi kulambila Mulungu kuti you are holy Lord there is no one like you kumwamba ndi dziko lapansi ndinu nokha.

CHOGWADA ( Luka 22 vs 41)
>Uku ndi kulapa machimo komanso kuzichepetsa kwa Mulungu ndikupereka Ulemu.

CHOGONA PANSI CHA FUFUMIMBA ( Matthews 26 vs 39)
>Uku kumasonyeza Ulemu wotheratu kwa Mulungu palibe ofanana nanu padziko lonse.

CHOKHALA PANSI ( Nehemiah 1 vs 4)

>Uku ndikumpempha Mulungu kuti ndiphunzitseni njira zanu ndi zaufumu wanu ndilipano baba. (1 Chronicles 17 vs 16).

*Healthy Herbal Care ☘️*

28/12/2025

*ENDOMETRIOSIS*

✍🏽Endometriosis ndi nthenda la zomatilira/zotupa zomwe timapezeka kunja ndi nkati mwa chibelekero, njira yodutsira mazira, kopezeka mazira komanso malo ena mthupi la munthu wa mkazi

Ili ndi vuto lomwe akazi ambiri akuvutika nalo. Nthawi zambiri amayesa kuti mwina ndi fibroids kapena ovarian cyst koma ayi akapanga scan samazipeza.

Ngati achipatala anakuuzani kuti mulibe fibroids komanso ovarian cysts koma mukuvutikabe ndi:

* Ululu nchiuno,
* Period yayitali pena yayifupi,
* Kupweteka pogonana,
* Kusabeleka,
* Kupweteka kodetsa nkhawa mwezi uliwonse.
* Kupweteka pokodza.
* Kutaya magazi ochuluka nthawi ya period.

Dziwani kuti ndi Endometriosis.

✓Zoyambitsa vutoli ndi zambiri, zina mwa izo ndi izi:

1. Kusapanga balance kwa ma hormones.
2. Kubwelera kwa magazi kupita ku njira zina mmalo motuluka kunja nthawi ya period.
3. Opaleshoni

*NOTE:*
Amayi ambiri akulephera kubeleka chifukwa cha vutoli. Mankhwala tilinawo mitundu iwiri

Mankhwala alipo othana ndi vutoli.

*Healthy Herbs Care ☘️*

Want your business to be the top-listed Beauty Salon in Lilongwe?
Click here to claim your Sponsored Listing.

Category

Website

Address


T/A Njolomole, Ntcheu
Lilongwe