Eveready Waste Cleaners
We collect Wastes in households, lodges, institution etc. at an agreed fee.
05/03/2026
16/08/2025
Quality Service, Quality Environment
01/03/2024
09/02/2024
Timatolela ma General Waste ma Nyumba, Lodges, School, Offices etc. Pa Nyumba ndi k8000 yokha basi pa Mwezi.
Clean Environment for All
05/02/2024
Tukamba za ma nyumba, lodges, offices etc
26/01/2024
Tiyeni tisamalile Town yathu posataya zinyalala mwachisawawa. Timatolela zinyalala ma lodge, ma xul, ma nyumba, ma office pa mtengo okambirana. Kma pa nyumba imodzi ndi k8000 per month.
12/01/2024
*Another Good Day that the Lord has given Us to Save and Beautify the Environment*
Ma nyumba anu, Zi ntchito, kuma business anu zinyanyala mutaya kuti? Ifeyo Timatolela zinyanyala pa Mtengo okambirana koma Per Household ndi k8000 per month.....
Click here to claim your Sponsored Listing.
Category
Contact the business
Website
Address
Liwonde-Machinga
Liwonde
