Chi Chi Beauty Parlour

Chi Chi Beauty Parlour

Share

Step into Stardom with Chi Chi Entertainment

Artist Management | Music Promotion | Live Events | Entertainment Sponsor | Record label | Artist Development

11/08/2026

Ma bride a weekend anali kawawa mwawona ozola kayera kuti akongoletsetse 🤣🤣🤣
Kaya nde Zavala ma dress angati can’t wait 💃🏼

09/08/2026

Congratulations the scorchers

09/08/2026
09/08/2026

Limbikirani nanunso pa ukwati wanu muzayende pa ndege ✈️🛬🛫
From waterfront to wine-lands

08/08/2026

Shout out to my newest followers! Excited to have you onboard!

Julia V Msasu, Doreen Chambo Chinkota, Pililani Baluti, Madalitso Mtukula, Liness Singano, Yamiecan Marquette, Loveness Boti, Billy Wisdom Jamu II, Vick Mw, Cathy Mvula, Olivia Zalira, Maduoma Adegoke, Pearl Tsholo, Jañet Nanyanga, Jashiley Das Martas, Gift Mwanyalih, Legitmate Husain, Ephelem Lucius

08/08/2026

Good morning

May this day be a great and miraculous day.Zisomo ndi zifundo zitipambanitse pa chili chonse chikutisowetsa Mtendere 🙏🏽.
Hugs 🤗

07/08/2026

Masalimo 3
Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero
Salimo la Davide. Atathawa mwana wake Abisalomu.

3 Inu Yehova, achulukadi adani anga!
Achulukadi amene andiwukira!
2 Ambiri akunena za ine kuti,
“Mulungu sadzamupulumutsa.”
Sela
3 Koma Inu Yehova, ndinu chishango chonditeteza,
Inu mwandiveka ulemerero ndipo mwanditukula.
4 Kwa Yehova, Ine ndilira mofuwula
ndipo Iye amandiyankha kuchokera ku phiri lake loyera.
Sela
5 Ine ndimagona ndi kupeza tulo;
ndimadzukanso chifukwa Yehova amandichirikiza.
6 Sindidzaopa adani anga osawerengeka amene
abwera kulimbana nane kuchokera ku madera onse.
7 Dzukani, Inu Yehova!
Pulumutseni, Inu Mulungu wanga.
Akantheni adani anga onse pa msagwada;
gululani mano a anthu oyipa.
8 Chipulumutso chimachokera kwa Yehova.
Madalitso akhale pa anthu anu.

06/08/2026

Nde kuli amuna or akazi oti ukapita nawo koyenda atenga ma number Atsikana/amuna ena munathana nawo bwanji anthu otelewa?

Want your business to be the top-listed Beauty Salon in Cape Town?
Click here to claim your Sponsored Listing.

Address


Cape Town
8005

Opening Hours

Monday 08:00 - 23:00
Tuesday 08:00 - 23:00
Wednesday 08:00 - 23:00
Thursday 08:00 - 23:00
Friday 08:00 - 23:00
Saturday 09:00 - 17:00